-
Ezara 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 M’chaka chachiwiri kuchokera pamene anabwera kunyumba ya Mulungu woona ku Yerusalemu, m’mwezi wachiwiri,+ Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli,+ Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki, abale awo onse, ansembe ndi Alevi, ndiponso anthu ena onse amene anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku ukapolo,+ anayamba kugwira ntchitoyo. Kenako anaika Alevi+ m’malo awo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo kuti akhale oyang’anira ntchito ya panyumba ya Yehova.+
-