1 Mafumu 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza. 1 Mafumu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuzungulira bwalo lalikulu panali khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuchokera pansi, ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Bwalo lamkati+ la nyumba+ ya Yehova ndi khonde+ la nyumbayo, zinamangidwanso mofanana. 2 Mbiri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu lamkati+ ndi zitseko za bwalo lalikululo. Zitsekozo anazikuta ndi mkuwa. 2 Mbiri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Yehosafati anaimirira pakati pa mpingo wa anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu, m’nyumba ya Yehova+ patsogolo pa bwalo latsopano,+
36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.
12 Kuzungulira bwalo lalikulu panali khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuchokera pansi, ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Bwalo lamkati+ la nyumba+ ya Yehova ndi khonde+ la nyumbayo, zinamangidwanso mofanana.
9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu lamkati+ ndi zitseko za bwalo lalikululo. Zitsekozo anazikuta ndi mkuwa.
5 Kenako Yehosafati anaimirira pakati pa mpingo wa anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu, m’nyumba ya Yehova+ patsogolo pa bwalo latsopano,+