Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+

  • 1 Mafumu 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno anayamba kulankhula kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ palibe Mulungu wina wofanana ndi inu+ kumwambako kapena pansi pano. Atumiki anu+ amene akuyenda pamaso panu ndi mtima wawo wonse,+ inu mumawasungira pangano ndi kukoma mtima kosatha.+

  • Aheberi 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anachita zimenezo kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, zimene chifukwa cha zinthu zimenezo n’zosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe kwambiri, kuti tigwire mwamphamvu chiyembekezo+ chimene chaikidwa patsogolo pathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena