Numeri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati umu ndi mmene muchitire ndi ine, ndikomereni mtima chonde, ingondiphani kuti tsokali lindichoke.”+ 1 Mafumu 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo iyeyo analowa m’chipululu n’kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Kenako anafika pa kamtengo kenakake,+ ndipo anakhala pansi pake. Ndiyeno anayamba kupempha kuti afe, ponena kuti: “Basi ndatopa nazo. Tsopano chotsani moyo wanga+ Yehova, pakuti sindine woposa makolo anga.” Yobu 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika? Yona 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+
15 Ngati umu ndi mmene muchitire ndi ine, ndikomereni mtima chonde, ingondiphani kuti tsokali lindichoke.”+
4 ndipo iyeyo analowa m’chipululu n’kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Kenako anafika pa kamtengo kenakake,+ ndipo anakhala pansi pake. Ndiyeno anayamba kupempha kuti afe, ponena kuti: “Basi ndatopa nazo. Tsopano chotsani moyo wanga+ Yehova, pakuti sindine woposa makolo anga.”
21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika?
3 Tsopano inu Yehova, chotsani moyo wanga,+ pakuti kuli bwino kuti ndife kusiyana n’kukhala ndi moyo.”+