Genesis 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ 1 Mbiri 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ketura+ mdzakazi*+ wa Abulahamu anabereka Zimirani, Yokesani, Medani,+ Midiyani,+ Isibaki,+ ndi Shuwa.+ Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+
2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
32 Ketura+ mdzakazi*+ wa Abulahamu anabereka Zimirani, Yokesani, Medani,+ Midiyani,+ Isibaki,+ ndi Shuwa.+ Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+