Hoseya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+ 2 Akorinto 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho n’zosadabwitsa ngati atumiki ake+ nawonso amadzisandutsa atumiki a chilungamo. Koma mapeto awo adzakhala monga mwa ntchito zawo.+ Tito 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino.
2 Mumtima mwawo saganiza+ kuti ine ndidzakumbukira zochita zawo zonse zoipa.+ Tsopano ntchito zawo zawazungulira+ ndipo zili pamaso panga.+
15 Choncho n’zosadabwitsa ngati atumiki ake+ nawonso amadzisandutsa atumiki a chilungamo. Koma mapeto awo adzakhala monga mwa ntchito zawo.+
16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino.