Salimo 69:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipulumutseni m’matope kuti ndisamire.+Ndipulumutseni kwa anthu odana nane+ ndiponso ku madzi akuya.+ Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+
14 Ndipulumutseni m’matope kuti ndisamire.+Ndipulumutseni kwa anthu odana nane+ ndiponso ku madzi akuya.+
6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+