Salimo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+ Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+ Salimo 102:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 102 Inu Yehova, imvani pemphero langa.+Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 130:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga Yehova.+Makutu anu amve mawu anga ochonderera.+
2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+