Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+ 1 Samueli 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Mawa nthawi ngati ino ndikutumizira munthu kuchokera kudera la Benjamini,+ ndipo udzam’dzoze+ kukhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli. Iye adzapulumutsa anthu anga m’manja mwa Afilisiti,+ chifukwa ndaona kusautsika kwawo ndipo ndamva kulira kwawo.”+ Salimo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 145:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anthu amene amamuopa adzawachitira zokhumba zawo,+Adzamva kufuula kwawo kopempha thandizo ndipo adzawapulumutsa.+
23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+
16 “Mawa nthawi ngati ino ndikutumizira munthu kuchokera kudera la Benjamini,+ ndipo udzam’dzoze+ kukhala mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli. Iye adzapulumutsa anthu anga m’manja mwa Afilisiti,+ chifukwa ndaona kusautsika kwawo ndipo ndamva kulira kwawo.”+
6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+
19 Ndipo anthu amene amamuopa adzawachitira zokhumba zawo,+Adzamva kufuula kwawo kopempha thandizo ndipo adzawapulumutsa.+