1 Samueli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti. 1 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+
5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti.
14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+