Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova anamva mawu a Aisiraeli, ndipo anapereka Akananiwo m’manja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. N’chifukwa chake malowo anawatcha Horima.*+

  • Yoswa 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Yehova anasokoneza adaniwo pamaso pa Aisiraeli.+ Ndiyeno Aisiraeli anayamba kupha adaniwo kwadzaoneni ku Gibeoni,+ ndi kuwathamangitsa kulowera kuchitunda cha Beti-horoni. Ndipo anapitiriza kuwapha mpaka kukafika ku Azeka+ ndi ku Makeda.+

  • Yeremiya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira kwa Iye.”’+ ‘Anthu onse ofuna kumumeza anali kukhala ndi mlandu+ ndipo tsoka linali kuwagwera,’ watero Yehova.”+

  • Yoweli 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Kalanga ine! Tsiku lija likufika.+ Tsiku la Yehova lili pafupi.+ Tsikulo lidzafika ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena