Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwabwino kuposa moyo,+Milomo yanga idzakuyamikirani.+ Salimo 109:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma inu ndinu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndikomereni mtima chifukwa cha dzina lanu.+Ndilanditseni,+ popeza kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwakukulu.
7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+
21 Koma inu ndinu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndikomereni mtima chifukwa cha dzina lanu.+Ndilanditseni,+ popeza kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwakukulu.