Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chitirani Ziyoni zabwino mwa kukoma mtima kwanu.+

      Ndipo mangani mpanda wa Yerusalemu.+

  • Yesaya 14:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kodi munthu adzawayankha chiyani amithenga+ a mitundu ya anthu? Adzawayankha kuti, Yehova waika maziko a Ziyoni,+ ndipo anthu ake osautsika adzathawira mmenemo.

  • Yesaya 44:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kukwaniritsidwa ndiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene atumiki anga analengeza.+ Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+ Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+ ndipo malo ake osakazidwa ndidzawamanganso.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena