Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+ Salimo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+
12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+
10 Ndinene ndi mtima wanga wonse kuti:+“Inu Yehova, ndani angafanane ndi inu,+Amene mumalanditsa wosautsika m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo,+Amene mumalanditsa wozunzika ndi wosauka m’manja mwa munthu amene akumulanda zinthu zake?”+