Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.

  • Yeremiya 49:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “‘Choncho taonani! Masiku adzafika,’ watero Yehova, ‘ndipo Raba,+ umene ndi mzinda wa ana a Amoni, ndidzaulizira chizindikiro chakuti kukubwera nkhondo.+ Ndipo mzindawu udzasanduka bwinja ndi mulu wadothi.+ Midzi yake yozungulira+ idzatenthedwa.’+

      “‘Isiraeli adzatenga dziko la anthu amene analanda dziko lake,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena