Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwa Arefai+ onse, Ogi yekha mfumu ya Basana ndi amene anali atatsala. Chithatha chimene anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo. Kodi si chija chili ku Raba+ wa ana a Aamoni? N’chachitali mikono* 9, ndipo m’lifupi mwake mikono inayi, kutsatira muyezo wodziwika.

  • Yoswa 13:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Gawo lawo linayambira kumzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi,+ ndi hafu ya dziko la ana a Amoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli+ kufupi ndi Raba.+

  • Ezekieli 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la ana a Amoni ndidzalisandutsa malo opumulirako gulu la nkhosa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+

  • Amosi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzayatsa mpanda wa Raba+ ndipo motowo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo. Padzakhala chizindikiro chochenjeza pa tsiku la nkhondo ndiponso mphepo yamkuntho pa tsiku la chimvula champhamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena