Deuteronomo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+ Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+