Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+ Salimo 69:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+
16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+
2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+