Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Pa tsiku lanu losangalala,+ pa nyengo ya zikondwerero zanu,+ ndi pa masiku oyambira miyezi,+ muziliza malipengawo popereka nsembe zanu zopsereza+ ndi zachiyanjano.+ Kuliza malipengawo kudzakhala chikumbutso kwa Mulungu wanu. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.”+

  • Numeri 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,

      Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.

      Mulungu wake Yehova ali naye,+

      Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.

  • Salimo 98:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Fuulani mwa kuimba malipenga ndi mphalasa.*+

      Fuulani mosangalala pamaso pa Mfumu Yehova, chifukwa wapambana.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena