Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Salimo 126:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene akukhetsa misozi pofesa mbewu,+Adzakolola akufuula mosangalala.+ Mateyu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Odala ndi anthu amene akumva chisoni, chifukwa adzasangalatsidwa.+ Yohane 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+