Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakati pa Ayuda panali chisangalalo, kukondwa+ ndi kunyadira ndipo anthu anali kuwapatsa ulemu.

  • Yobu 22:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zimene waganiza kuti uchite zidzatheka,

      Ndipo kuwala kudzaunikira njira zako.+

  • Salimo 112:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+

      ח [Chehth]

      Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+

  • Miyambo 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma njira ya olungama ili ngati kuwala kwamphamvu kumene kumamka kuwonjezereka mpaka tsiku litakhazikika.+

  • Yesaya 30:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kuwala kwa mwezi wathunthu kudzakhala ngati kuwala kwa dzuwa lowala kwambiri. Kuwala kwa dzuwa lowala kwambiri kudzawonjezereka maulendo 7+ ndipo kudzakhala ngati kuwala kwa masiku 7. Zimenezi zidzachitika m’tsiku limene Yehova adzachiritse mtundu wake wovulala+ ndi kupoletsa+ chilonda choopsa cha anthu ake, amene iyeyo anawavulaza powalanga.

  • Mika 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mkwiyo waukulu wa Yehova ndiupirira chifukwa ndamuchimwira.+ Ndiupirirabe kufikira ataweruza mlandu wanga mondikomera ndi kundichitira chilungamo.+ Iye adzandipititsa pamalo owala ndipo ndidzaona kulungama kwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena