Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 60:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+

  • Habakuku 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kuwala kwake kunali ngati kuwala kwa masana.+ Kuwala kwa mitundu iwiri kunali kutuluka m’dzanja lake ndipo m’dzanja lakemo ndi mmene munali kubisala mphamvu zake.+

  • Habakuku 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kumwamba,+ dzuwa ndi mwezi zinaima.+ Mivi yanu inapitiriza kuyenda ngati kuwala.+ Kunyezimira kwa mkondo wanu kunakhala ngati kuwala kounikira.+

  • Chivumbulutso 21:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mzindawo sunafunikirenso kuwala kwa dzuwa kapena kwa mwezi, pakuti ulemerero wa Mulungu unauwalitsa,+ ndipo nyale yake inali Mwanawankhosa.+

  • Chivumbulutso 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso.+ Sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo adzalamulira monga mafumu kwamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena