Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Deuteronomo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira. Luka 1:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Iye wathandiza mtumiki wake Isiraeli.+ Wachita zimenezi posonyeza kuti akukumbukira lonjezo lake lakuti adzasonyeza chifundo kwamuyaya,+
42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.
31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira.
54 Iye wathandiza mtumiki wake Isiraeli.+ Wachita zimenezi posonyeza kuti akukumbukira lonjezo lake lakuti adzasonyeza chifundo kwamuyaya,+