Oweruza 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patapita nthawi, mwamuna wina wokalamba anatulukira madzulowo+ akuchokera ku ntchito yake ya kumunda. Kwawo kwa mwamunayo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali kukhala ku Gibeya kwa kanthawi, koma amuna a mumzindawo anali Abenjamini.+ 2 Atesalonika 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+
16 Patapita nthawi, mwamuna wina wokalamba anatulukira madzulowo+ akuchokera ku ntchito yake ya kumunda. Kwawo kwa mwamunayo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali kukhala ku Gibeya kwa kanthawi, koma amuna a mumzindawo anali Abenjamini.+
8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+