Deuteronomo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola.+ N’chifukwa chake lero ndikukulamula zinthu zimenezi. Salimo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuikiza mzimu* wanga m’manja mwanu.+Mwandiwombola,+ inu Yehova, Mulungu wachoonadi.+ Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+ 1 Petulo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+
15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola.+ N’chifukwa chake lero ndikukulamula zinthu zimenezi.
68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+
19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+