Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+

  • Miyambo 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakhutira ndi zotsatira za njira zake,+ koma munthu wabwino adzakhutira ndi zotsatira za zochita zake.+

  • Ezekieli 35:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Chotero pali ine Mulungu wamoyo, mlandu wa magazi udzakutsatira chifukwa ndinakonza zoti magazi ako akhetsedwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Ndithudi iwe unadana ndi amene unakhetsa magazi awo, choncho mlandu wa magazi udzakutsatira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena