Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+

  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+

  • Salimo 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+

      Pakuti Yehova ali pakati pa khamu* la anthu olungama.+

  • Salimo 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Umenewo ndiwo m’badwo wa amene amafunafuna Mulungu,

      M’badwo wa anthu ofunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena