Ekisodo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja. Yoswa 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tinamva za mmene Yehova anaphwetsera madzi a Nyanja Yofiira pamaso panu, mutatuluka m’dziko la Iguputo.+ Tinamvanso za mmene munaphera+ mafumu awiri a Aamori, Sihoni+ ndi Ogi,+ kutsidya kwa Yorodano. Habakuku 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+
8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja.
10 Tinamva za mmene Yehova anaphwetsera madzi a Nyanja Yofiira pamaso panu, mutatuluka m’dziko la Iguputo.+ Tinamvanso za mmene munaphera+ mafumu awiri a Aamori, Sihoni+ ndi Ogi,+ kutsidya kwa Yorodano.
8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+