Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Tsopano Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake.+ Umuchite zimene unachitira Sihoni mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.”+

  • Deuteronomo 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Yehova Mulungu wathu anaperekanso Ogi mfumu ya Basana ndi anthu ake onse m’manja mwathu, ndipo tinam’kantha moti sipanatsale ndi mmodzi yemwe wopulumuka mwa anthu ake.+

  • Yoswa 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina la Yorodano. Mafumuwo ndiwo Sihoni+ mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali ku Asitaroti.+

  • Salimo 135:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+

      Ndi Ogi mfumu ya Basana,+

      Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena