Yesaya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’tsiku limenelo,+ padzakhala muzu wa Jese+ womwe udzaimirire ngati chizindikiro kwa anthu.+ Ngakhale anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awatsogolere,+ ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.+ Yesaya 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aliyense adzakhala ngati malo obisalirapo mphepo ndi malo ousapo mvula yamkuntho,+ ngati mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,+ ndiponso ngati mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma.+ Aroma 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Inetu ndikuika mwala+ wopunthwitsa ndiponso mwala wokhumudwitsa+ m’Ziyoni, koma munthu wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”+
10 M’tsiku limenelo,+ padzakhala muzu wa Jese+ womwe udzaimirire ngati chizindikiro kwa anthu.+ Ngakhale anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awatsogolere,+ ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.+
2 Aliyense adzakhala ngati malo obisalirapo mphepo ndi malo ousapo mvula yamkuntho,+ ngati mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,+ ndiponso ngati mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma.+
33 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Inetu ndikuika mwala+ wopunthwitsa ndiponso mwala wokhumudwitsa+ m’Ziyoni, koma munthu wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”+