Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.

  • 1 Mafumu 8:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la atumiki anu, anthu anu Aisiraeli, popeza mumawaphunzitsa+ njira yabwino yoti ayendemo.+ Mubweretse mvula+ padziko lanu, limene mwapatsa anthu anu monga cholowa.

  • Salimo 86:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+

      Ndidzayenda m’choonadi chanu.+

      Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+

  • Yesaya 30:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yehova adzakupatsani masautso kuti akhale chakudya chanu, ndiponso adzakupatsani kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa.+ Koma Mlangizi wako Wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso ako adzayamba kuona Mlangizi wako Wamkulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena