Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 119:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Odala ndi anthu osalakwitsa kanthu m’njira zawo,+Anthu amene akutsatira chilamulo cha Yehova.+ Salimo 119:142 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 142 Chilungamo chanu ndi chilungamo mpaka kalekale,+Ndipo chilamulo chanu ndi choonadi.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+