Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndikumva chisoni+ kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye watembenuka,+ wasiya kunditsatira, ndipo sakumvera mawu anga.”+ Samueli anavutika maganizo kwambiri ndi nkhani imeneyi+ moti anafuulira Yehova usiku wonse.+

  • Yeremiya 9:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 kuti abwere mofulumira ndi kudzatiimbira nyimbo zoimba polira. Maso athu atuluke misozi, madzi atuluke m’maso athu owala.+

  • Maliro 3:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Maso anga akungotuluka misozi ngati mtsinje chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+

  • 2 Petulo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Munthu wolungama ameneyo anali kuzunzika tsiku ndi tsiku ndi zimene anali kuona ndi kumva pamene anali kukhala pakati pawo, ndiponso chifukwa cha zochita zawo zosamvera malamulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena