Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  53 Mkwiyo ukuyaka mumtima mwanga chifukwa cha oipa,+

      Amene akusiya chilamulo chanu.+

  • Ezekieli 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Yehova anauza munthu uja kuti: “Uyendeyende mumzinda wonse wa Yerusalemu, ndipo ulembe chizindikiro pamphumi za anthu amene akuusa moyo* ndi kubuula+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene zikuchitika mumzindawu.”+

  • Ezekieli 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+

  • Hoseya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+

  • Amosi 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Yuda+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anakana lamulo la Yehova+ ndiponso sanasunge malangizo ake koma anasocheretsedwa ndi mabodza+ amene makolo awo anali kutsatira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena