Salimo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzadzikonzera zida za imfa,+Ndipo adzapanga mivi yake kukhala yoyaka moto walawilawi.+ Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+ Salimo 64:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+
3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+