Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yuda wakhala kapolo chifukwa cha nsautso+ ndiponso chifukwa cha kukula kwa ntchito yaukapolo imene akugwira.+

      Iye wakhala pakati pa mitundu ina ya anthu,+ ndipo sanapeze malo ampumulo.

      Onse amene anali kumuzunza amupeza pa nthawi ya mavuto ake.+

  • Ezekieli 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Akazi amenewa anayamba kuchita uhule m’dziko la Iguputo.+ Anayamba uhule umenewu ali atsikana ang’onoang’ono.+ Kumeneko amuna anafinya mabere awo+ ndi kutsamira chifuwa chawo ali anamwali.

  • Hoseya 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pa nthawi imene Isiraeli anali mnyamata ndinamukonda,+ ndipo ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena