Yobu 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amauza Mulungu woona kuti, ‘Chokani kwa ife!+Sitikufuna kudziwa njira zanu.+ Salimo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+ Salimo 73:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amanyodola ndi kulankhula zinthu zoipa.+Amalankhula za chinyengo chawo modzikweza.+ Miyambo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Aliyense wokonzera anzake ziwembu adzatchedwa katswiri wa maganizo oipa.+