Salimo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+ Miyambo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+ Miyambo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wabwino Yehova amakondwera naye,+ koma munthu wamaganizo oipa iye amamutcha woipa.+ Aroma 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ndi miseche.+ Anakhala odana ndi Mulungu, achipongwe,+ odzikweza,+ odzimva,+ oyambitsa zoipa,+ osamvera makolo,+
14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+
30 ndi miseche.+ Anakhala odana ndi Mulungu, achipongwe,+ odzikweza,+ odzimva,+ oyambitsa zoipa,+ osamvera makolo,+