Salimo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sapereka ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+Wochita zinthu zimenezi, sadzagwedezeka konse.+ Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
5 Sapereka ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+Wochita zinthu zimenezi, sadzagwedezeka konse.+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+