Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno chifukwa chakuti mitima yawo inali yosangalala,+ anayamba kunena kuti: “Itanani Samisoni kuti adzatisangalatse.”+ Chotero anaitana Samisoni ndipo anam’tulutsa m’ndende kuti awachitire masewera.+ Atabwera anamuimiritsa pakati pa zipilala.

  • 2 Samueli 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+

  • Yobu 31:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ngati ndinkasangalala ndi kutha kwa munthu amene ankadana nane kwambiri,+

      Kapena ngati ndinkakondwera chifukwa chakuti zoipa zam’gwera . . .

  • Miyambo 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Wonyoza munthu wosauka amanyoza amene anam’panga.+ Amene amasangalala ndi tsoka la wina sadzalephera kulangidwa.+

  • Miyambo 25:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ngati munthu wodana nawe ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse madzi akumwa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena