1 Samueli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+ 1 Samueli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+
18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+
7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+