Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+ Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+ Aefeso 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano, kodi mawu akuti “anakwera kumwamba”+ amatanthauza chiyani? Amatanthauza kuti anayamba watsika pansi, padziko.+
13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+
9 Tsopano, kodi mawu akuti “anakwera kumwamba”+ amatanthauza chiyani? Amatanthauza kuti anayamba watsika pansi, padziko.+