Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, tamvera malangizo a bambo ako,+ ndipo usasiye malamulo a mayi ako,+ Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, sunga lamulo la bambo ako,+ ndipo usasiye malangizo a mayi ako.+ 2 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti ndikukumbukira chikhulupiriro+ chopanda chinyengo+ chimene uli nacho, chimene chinayamba kukhazikika mwa agogo ako aakazi a Loisi, ndi mayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti chilinso mwa iwe. 2 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+
5 Pakuti ndikukumbukira chikhulupiriro+ chopanda chinyengo+ chimene uli nacho, chimene chinayamba kukhazikika mwa agogo ako aakazi a Loisi, ndi mayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti chilinso mwa iwe.
15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+