Miyambo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upeze nzeru,+ upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa mawu a m’kamwa mwanga.+ Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+ Miyambo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+ Mlaliki 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kumvetsera munthu wanzeru akamakudzudzula,+ kusiyana ndi kumvetsera nyimbo ya anthu opusa.+ Mateyu 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo. Luka 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Yesetsani+ mwamphamvu kulowa pakhomo lopapatiza.+ Chifukwa ambiri ndikukuuzani, adzafunitsitsa kulowamo koma sadzatha.+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+
5 Kuli bwino kumvetsera munthu wanzeru akamakudzudzula,+ kusiyana ndi kumvetsera nyimbo ya anthu opusa.+
13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo.
24 “Yesetsani+ mwamphamvu kulowa pakhomo lopapatiza.+ Chifukwa ambiri ndikukuuzani, adzafunitsitsa kulowamo koma sadzatha.+