1 Samueli 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zitatero Sauli anauza Mikala kuti: “N’chifukwa chiyani wandipusitsa+ chotere mwa kuthawitsa mdani wanga+ kuti apulumuke?” Poyankha, Mikala anauza Sauli kuti: “Iyeyo anandiuza kuti, ‘Ndilole ndipite! Apo ayi, ndikupha.’” Nehemiya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anamulemba ganyu+ n’cholinga choti ndichite mantha+ kuti ndikalowe m’kachisi ndi kuchimwa.+ Mwakutero, akanandiipitsira dzina langa+ kuti azindinyoza.+
17 Zitatero Sauli anauza Mikala kuti: “N’chifukwa chiyani wandipusitsa+ chotere mwa kuthawitsa mdani wanga+ kuti apulumuke?” Poyankha, Mikala anauza Sauli kuti: “Iyeyo anandiuza kuti, ‘Ndilole ndipite! Apo ayi, ndikupha.’”
13 Iwo anamulemba ganyu+ n’cholinga choti ndichite mantha+ kuti ndikalowe m’kachisi ndi kuchimwa.+ Mwakutero, akanandiipitsira dzina langa+ kuti azindinyoza.+