Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+

  • 2 Samueli 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano panali munthu wina wopanda pake+ dzina lake Sheba,+ mwana wamwamuna wa Bikiri, wafuko la Benjamini. Iye analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi kunena kuti: “Tilibe gawo mwa Davide, ndipo tilibe cholowa mwa mwana wa Jese.+ Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu+ yake!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena