Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iyeyu atafika anapempha kuti, ‘Chonde ndikunkheko.+ Ndizitola balere wotsala m’mbuyo mwa okololawo.’ Atatero, analowa m’mundamu n’kuyamba kukunkha. Wakhala akukunkha kuyambira m’mawa mpaka posachedwapa pamene anakhala pansi pang’ono m’chisimbamu.”*+

  • 2 Mafumu 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mayi wina yemwe anali mmodzi wa akazi a ana+ a aneneri, anafika kwa Elisa n’kulankhula mokweza kuti: “Mtumiki wanu yemwe anali mwamuna wanga anamwalira. Inu mukudziwa bwino kuti mtumiki wanuyo anali woopa+ Yehova. Tsopano kwabwera wangongole+ kudzatenga ana anga onse awiri kuti akakhale akapolo ake.”

  • Yakobo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena