Salimo 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova, sokonezani anthu oipa, ndipo sokonezani zonena zawo,+Pakuti ndaona ziwawa ndi mikangano mumzinda.+ Mlaliki 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+ Yeremiya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amakunga lilime lawo ngati uta kuti aponye chinyengo,+ koma iwo si okhulupirika m’dzikoli. “Iwo anali kuchita zoipa motsatizanatsatizana ndipo anandinyalanyaza,”+ watero Yehova. Hoseya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+
9 Inu Yehova, sokonezani anthu oipa, ndipo sokonezani zonena zawo,+Pakuti ndaona ziwawa ndi mikangano mumzinda.+
14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
3 Iwo amakunga lilime lawo ngati uta kuti aponye chinyengo,+ koma iwo si okhulupirika m’dzikoli. “Iwo anali kuchita zoipa motsatizanatsatizana ndipo anandinyalanyaza,”+ watero Yehova.
2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+