Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 9:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane,+ ataona zimenezi anati: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto+ kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”

  • Yakobo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.

  • Yakobo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena