Miyambo 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense wochenjera amachita zinthu mozindikira,+ koma wopusa amafalitsa uchitsiru.+ Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa m’pamene pamamuwononga,+ ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.+ Miyambo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wopusa amatulutsa mkwiyo* wake wonse, koma wanzeru amakhala wodekha mpaka pamapeto.+ Mlaliki 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti maloto amabwera chifukwa chochuluka zochita,+ ndipo kuchuluka kwa mawu kumachititsa munthu kulankhula zinthu zopusa.+
3 Pakuti maloto amabwera chifukwa chochuluka zochita,+ ndipo kuchuluka kwa mawu kumachititsa munthu kulankhula zinthu zopusa.+